-
2 Akorinto 4:1, 2Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
4 Choncho, popeza tili ndi utumiki umenewu mogwirizana ndi chifundo chimene tinasonyezedwa, sitikutaya mtima. 2 Koma tasiya zinthu zochititsa manyazi zochitikira mseri, ndipo sitikuyenda mwachinyengo kapena kupotoza mawu a Mulungu.+ Koma pochititsa choonadi kuti chidziwike, takhala chitsanzo chabwino kwa munthu* aliyense pamaso pa Mulungu.+
-