1 Akorinto 2:4, 5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Polankhula ndiponso polalikira, mawu anga sanali okopa kapena osonyeza nzeru, koma oonetsa mzimu ndi mphamvu,+ 5 kuti musamakhulupirire nzeru za anthu koma mphamvu ya Mulungu.
4 Polankhula ndiponso polalikira, mawu anga sanali okopa kapena osonyeza nzeru, koma oonetsa mzimu ndi mphamvu,+ 5 kuti musamakhulupirire nzeru za anthu koma mphamvu ya Mulungu.