2 Akorinto 10:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Zida zimene tikumenyera nkhondoyi si zamʼdzikoli,+ koma ndi zida zamphamvu zimene Mulungu+ watipatsa ndipo zimatha kugwetsa zinthu zozikika molimba. Aefeso 6:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Valani zida zonse zankhondo+ zochokera kwa Mulungu kuti musagonje polimbana ndi zochita zachinyengo* za Mdyerekezi,
4 Zida zimene tikumenyera nkhondoyi si zamʼdzikoli,+ koma ndi zida zamphamvu zimene Mulungu+ watipatsa ndipo zimatha kugwetsa zinthu zozikika molimba.
11 Valani zida zonse zankhondo+ zochokera kwa Mulungu kuti musagonje polimbana ndi zochita zachinyengo* za Mdyerekezi,