Aroma 13:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Usiku uli pafupi kutha ndipo masana ayandikira. Choncho tiyeni tivule ntchito za mdima+ ndipo tivale zida za kuwala.+
12 Usiku uli pafupi kutha ndipo masana ayandikira. Choncho tiyeni tivule ntchito za mdima+ ndipo tivale zida za kuwala.+