2 Akorinto 12:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Koma ineyo ndidzagwiritsa ntchito zinthu zanga zonse komanso ndidzadzipereka ndi mtima wanga wonse chifukwa cha inu, ndipo ndidzachita zimenezi mosangalala.+ Ngati ineyo ndimakukondani kwambiri chonchi, kodi inuyo mukuyenera kundikonda pangʼono?
15 Koma ineyo ndidzagwiritsa ntchito zinthu zanga zonse komanso ndidzadzipereka ndi mtima wanga wonse chifukwa cha inu, ndipo ndidzachita zimenezi mosangalala.+ Ngati ineyo ndimakukondani kwambiri chonchi, kodi inuyo mukuyenera kundikonda pangʼono?