Yakobo 4:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Achigololo inu,* kodi simukudziwa kuti kuchita ubwenzi ndi dziko nʼkudziika pa udani ndi Mulungu? Choncho aliyense amene akufuna kukhala bwenzi la dziko akudzipangitsa kuti akhale mdani wa Mulungu.+
4 Achigololo inu,* kodi simukudziwa kuti kuchita ubwenzi ndi dziko nʼkudziika pa udani ndi Mulungu? Choncho aliyense amene akufuna kukhala bwenzi la dziko akudzipangitsa kuti akhale mdani wa Mulungu.+