Machitidwe 11:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Choncho ophunzirawo anatsimikiza mtima kutumiza thandizo+ kwa abale a ku Yudeya, aliyense mogwirizana ndi zimene akanakwanitsa.+ 2 Akorinto 9:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Aliyense achite mogwirizana ndi mmene watsimikizira mumtima mwake, osati monyinyirika kapena mokakamizika,+ chifukwa Mulungu amakonda munthu amene amapereka mosangalala.+
29 Choncho ophunzirawo anatsimikiza mtima kutumiza thandizo+ kwa abale a ku Yudeya, aliyense mogwirizana ndi zimene akanakwanitsa.+
7 Aliyense achite mogwirizana ndi mmene watsimikizira mumtima mwake, osati monyinyirika kapena mokakamizika,+ chifukwa Mulungu amakonda munthu amene amapereka mosangalala.+