1 Petulo 1:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Popeza mwadziyeretsa pokhala omvera choonadi cha mʼMawu a Mulungu ndipo tsopano mumakonda abale mopanda chinyengo,+ muzikondana kwambiri kuchokera mumtima.+ 1 Petulo 2:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Muzilemekeza anthu amitundu yonse.+ Muzikonda gulu lonse la abale,+ muziopa Mulungu+ komanso muzilemekeza mfumu.+
22 Popeza mwadziyeretsa pokhala omvera choonadi cha mʼMawu a Mulungu ndipo tsopano mumakonda abale mopanda chinyengo,+ muzikondana kwambiri kuchokera mumtima.+
17 Muzilemekeza anthu amitundu yonse.+ Muzikonda gulu lonse la abale,+ muziopa Mulungu+ komanso muzilemekeza mfumu.+