Yohane 1:42 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 42 ndipo anapita naye kwa Yesu. Yesu atamuyangʼana anati: “Iwe ndiwe Simoni+ mwana wa Yohane, dzina lako likhala Kefa” (limene kumasulira kwake ndi “Petulo”).+ 1 Akorinto 15:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Panalinso zoti anaonekera kwa Kefa,*+ kenako kwa atumwi 12 aja.+
42 ndipo anapita naye kwa Yesu. Yesu atamuyangʼana anati: “Iwe ndiwe Simoni+ mwana wa Yohane, dzina lako likhala Kefa” (limene kumasulira kwake ndi “Petulo”).+