Aroma 8:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Komatu si zokhazi. Ifeyo amene tili ndi zipatso zoyambirira zomwe ndi mzimu, tikubuula mumtima mwathu+ pamene tikudikira ndi mtima wonse kuti Mulungu atitenge kukhala ana ake,+ kutimasula ndi dipo* ku matupi athuwa.
23 Komatu si zokhazi. Ifeyo amene tili ndi zipatso zoyambirira zomwe ndi mzimu, tikubuula mumtima mwathu+ pamene tikudikira ndi mtima wonse kuti Mulungu atitenge kukhala ana ake,+ kutimasula ndi dipo* ku matupi athuwa.