Aroma 12:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Musamatengere* nzeru za nthawi* ino, koma khalani munthu watsopano posintha kwambiri maganizo anu,+ kuti muzindikire chifuniro cha Mulungu,+ chabwino, chovomerezeka ndi changwiro. 1 Atesalonika 4:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Mulungu akufuna kuti mukhale oyera+ komanso kuti muzipewa chiwerewere.*+ 1 Petulo 4:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Anachita zimenezi kuti pa nthawi yonse imene ali moyo asamachite zofuna za anthu+ koma za Mulungu.+
2 Musamatengere* nzeru za nthawi* ino, koma khalani munthu watsopano posintha kwambiri maganizo anu,+ kuti muzindikire chifuniro cha Mulungu,+ chabwino, chovomerezeka ndi changwiro.
2 Anachita zimenezi kuti pa nthawi yonse imene ali moyo asamachite zofuna za anthu+ koma za Mulungu.+