Akolose 3:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Inu akapolo, muzimvera anthu amene ndi ambuye anu+ pa zinthu zonse, osati pokhapokha pamene akukuonani pongofuna kusangalatsa anthu,* koma moona mtima ndiponso moopa Yehova.*
22 Inu akapolo, muzimvera anthu amene ndi ambuye anu+ pa zinthu zonse, osati pokhapokha pamene akukuonani pongofuna kusangalatsa anthu,* koma moona mtima ndiponso moopa Yehova.*