-
Aefeso 6:5, 6Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
5 Akapolo inu, muzimvera anthu amene ndi ambuye anu.+ Muziwaopa ndi kuwalemekeza kuchokera pansi pa mtima, ngati mmene mumachitira ndi Khristu. 6 Musamachite zimenezi pokhapokha pamene anthu akukuonani pongofuna kuwasangalatsa,*+ koma ngati akapolo a Khristu amene akuchita chifuniro cha Mulungu ndi mtima wonse.+
-