-
1 Akorinto 6:9-11Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
9 Kodi zoonadi inu simukudziwa kuti anthu osalungama sadzalowa mu Ufumu wa Mulungu?+ Musapusitsidwe.* Achiwerewere,*+ olambira mafano,+ achigololo,+ amuna amene amalola kugonedwa ndi amuna anzawo,+ amuna ogona amuna anzawo,+ 10 akuba, adyera,+ zidakwa,+ olalata, kapena olanda, onsewo sadzalowa mu Ufumu wa Mulungu.+ 11 Ndipo ena a inu munali otero. Koma mwasambitsidwa kukhala oyera,+ mwapatulidwa,+ mukuonedwa ngati olungama+ mʼdzina la Ambuye wathu Yesu Khristu, komanso ndi mzimu wa Mulungu wathu.
-