Aroma 5:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Koma Mulungu akutisonyeza chikondi chake, chifukwa pamene tinali ochimwa, Khristu anatifera.+ 1 Yohane 4:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Zimene Mulungu anachita potisonyeza chikondi chake ndi izi: Anatumiza Mwana wake wobadwa yekha+ mʼdzikoli kuti tidzapeze moyo wosatha kudzera mwa iye.+ 1 Yohane 4:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Ife timasonyeza chikondi, chifukwa Mulungu ndi amene anayamba kutikonda.+
9 Zimene Mulungu anachita potisonyeza chikondi chake ndi izi: Anatumiza Mwana wake wobadwa yekha+ mʼdzikoli kuti tidzapeze moyo wosatha kudzera mwa iye.+