Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yesaya 53:12
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 12 Pa chifukwa chimenechi, ndidzamupatsa gawo pamodzi ndi ambiri,

      Ndipo iye adzagawana ndi amphamvu katundu amene alanda kunkhondo,

      Chifukwa anapereka moyo wake*+

      Ndipo anaikidwa mʼgulu la anthu ochimwa.+

      Ananyamula tchimo la anthu ambiri+

      Ndipo analowererapo kuti athandize anthu ochimwa.+

  • Yohane 3:16
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 16 Chifukwa Mulungu anakonda kwambiri dziko moti anapereka Mwana wake wobadwa yekha,+ kuti aliyense womukhulupirira asawonongedwe koma akhale ndi moyo wosatha.+

  • Aefeso 2:4, 5
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 4 Koma popeza kuti Mulungu ndi wachifundo chochuluka,+ komanso chifukwa cha chikondi chake chachikulu chimene anatisonyeza,+ 5 anapangitsa kuti tikhale amoyo limodzi ndi Khristu, ngakhale kuti tinali akufa chifukwa cha machimo athu,+ ndipotu inu mwapulumutsidwa chifukwa cha kukoma mtima kwakukulu.

  • 1 Petulo 3:18
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 18 Pajatu ngakhale Khristu anafa kamodzi kokha kuti achotse uchimo.+ Munthu wolungamayo anafera anthu osalungama+ kuti akugwirizanitseni ndi Mulungu.+ Iye anaphedwa monga munthu,*+ koma anaukitsidwa monga mzimu.+

  • 1 Yohane 4:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Mulungu anatumiza Mwana wake monga nsembe yophimba+ machimo athu.*+ Anachita zimenezi chifukwa chakuti anatikonda, osati chifukwa choti ifeyo ndi amene tinamukonda.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena