-
Aefeso 1:3, 4Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
3 Atamandike Mulungu amene ndi Atate wa Ambuye wathu Yesu Khristu, chifukwa watidalitsa ndi dalitso lililonse lauzimu mʼmalo akumwamba mogwirizana ndi Khristu.+ 4 Iye anatisankha kuti tikakhale ogwirizana ndi Khristu dziko lisanakhazikitsidwe nʼcholinga choti tizisonyeza chikondi komanso kuti tikhale oyera ndiponso opanda chilema+ pamaso pa Mulungu.
-