Yesaya 65:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 65 “Ine ndalola kuti anthu amene sanafunse za ine andifunefune.Ndalola kuti anthu amene sanandifunefune andipeze.+ Mtundu umene sunaitane pa dzina langa ndauuza kuti, ‘Ndili pano, ndili pano!’+
65 “Ine ndalola kuti anthu amene sanafunse za ine andifunefune.Ndalola kuti anthu amene sanandifunefune andipeze.+ Mtundu umene sunaitane pa dzina langa ndauuza kuti, ‘Ndili pano, ndili pano!’+