-
1 Timoteyo 1:13, 14Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
13 Anatero ngakhale kuti kale ndinali wonyoza Mulungu, wozunza anthu ake ndiponso wachipongwe.+ Komabe anandichitira chifundo chifukwa ndinkachita zinthu mosadziwa komanso ndinalibe chikhulupiriro. 14 Koma ndinalandira kukoma mtima kwakukulu kwa Mulungu Ambuye wathu. Ndinalandiranso chikhulupiriro ndi chikondi cha Khristu Yesu.
-