Aefeso 1:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 amene chifukwa chogwirizana naye tinasankhidwa kuti tidzalandire cholowa,+ chifukwa anatisankha kale mwa kufuna kwake, iye amene amachita zinthu zonse mogwirizana ndi chifuniro chake.
11 amene chifukwa chogwirizana naye tinasankhidwa kuti tidzalandire cholowa,+ chifukwa anatisankha kale mwa kufuna kwake, iye amene amachita zinthu zonse mogwirizana ndi chifuniro chake.