Aroma 8:35 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 35 Ndani adzatisiyanitsa ndi chikondi cha Khristu?+ Kodi ndi masautso, zowawa, kuzunzidwa, njala, usiwa, zoopsa kapena lupanga?+
35 Ndani adzatisiyanitsa ndi chikondi cha Khristu?+ Kodi ndi masautso, zowawa, kuzunzidwa, njala, usiwa, zoopsa kapena lupanga?+