1 Timoteyo 6:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Nʼzoona kuti kukhala wodzipereka kwa Mulungu+ komanso kukhala wokhutira ndi zimene tili nazo, ndi njira yopezera phindu lalikulu. 1 Timoteyo 6:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Choncho, ngati tili ndi chakudya, zovala ndi pogona, tizikhala okhutira ndi zinthu zimenezi.+ Aheberi 13:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Musamakonde ndalama,+ koma muzikhutira ndi zimene muli nazo pa nthawiyo.+ Chifukwa Mulungu anati: “Sindidzakusiyani kapena kukutayani ngakhale pangʼono.”+
6 Nʼzoona kuti kukhala wodzipereka kwa Mulungu+ komanso kukhala wokhutira ndi zimene tili nazo, ndi njira yopezera phindu lalikulu.
5 Musamakonde ndalama,+ koma muzikhutira ndi zimene muli nazo pa nthawiyo.+ Chifukwa Mulungu anati: “Sindidzakusiyani kapena kukutayani ngakhale pangʼono.”+