Afilipi 1:12, 13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Tsopano abale, ndikufuna mudziwe kuti zimene zandichitikira, zathandiza kuti uthenga wabwino ufalikire. 13 Chifukwa Asilikali Oteteza Mfumu ndi ena onse amva+ kuti ndamangidwa+ chifukwa cha Khristu.
12 Tsopano abale, ndikufuna mudziwe kuti zimene zandichitikira, zathandiza kuti uthenga wabwino ufalikire. 13 Chifukwa Asilikali Oteteza Mfumu ndi ena onse amva+ kuti ndamangidwa+ chifukwa cha Khristu.