Afilipi 1:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Tsopano abale, ndikufuna mudziwe kuti zondichitikira zija, zathandiza kupititsa patsogolo uthenga wabwino+ m’malo moulepheretsa.
12 Tsopano abale, ndikufuna mudziwe kuti zondichitikira zija, zathandiza kupititsa patsogolo uthenga wabwino+ m’malo moulepheretsa.