1 Atesalonika 3:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Komanso, Ambuye akuthandizeni kuti muzikondana kwambiri ndiponso kuti muzikonda anthu ena+ ngati mmene ife timakukonderani.
12 Komanso, Ambuye akuthandizeni kuti muzikondana kwambiri ndiponso kuti muzikonda anthu ena+ ngati mmene ife timakukonderani.