1 Atesalonika 4:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Koma zokhudza kukonda abale,+ nʼzosafunika kuti tichite kukulemberani chifukwa inuyo, Mulungu amakuphunzitsani kuti muzikondana.+ 2 Atesalonika 1:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Tikuyenera kumathokoza Mulungu nthawi zonse chifukwa cha inu abale. Zimenezi nʼzoyenera chifukwa chikhulupiriro chanu chikukula kwambiri ndipo chikondi chimene aliyense amasonyeza kwa mnzake chikuwonjezereka.+
9 Koma zokhudza kukonda abale,+ nʼzosafunika kuti tichite kukulemberani chifukwa inuyo, Mulungu amakuphunzitsani kuti muzikondana.+
3 Tikuyenera kumathokoza Mulungu nthawi zonse chifukwa cha inu abale. Zimenezi nʼzoyenera chifukwa chikhulupiriro chanu chikukula kwambiri ndipo chikondi chimene aliyense amasonyeza kwa mnzake chikuwonjezereka.+