1 Akorinto 14:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Abale, musakhale ana aangʼono pa nkhani yomvetsa zinthu.+ Koma khalani ana pa zoipa,+ ndipo pa nkhani yomvetsa zinthu khalani anthu akuluakulu.+ Aheberi 5:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Koma chakudya chotafuna ndi cha anthu aakulu mwauzimu, amene amatha kusiyanitsa zoyenera ndi zosayenera chifukwa choti amagwiritsa ntchito luso lawo la kuganiza.*
20 Abale, musakhale ana aangʼono pa nkhani yomvetsa zinthu.+ Koma khalani ana pa zoipa,+ ndipo pa nkhani yomvetsa zinthu khalani anthu akuluakulu.+
14 Koma chakudya chotafuna ndi cha anthu aakulu mwauzimu, amene amatha kusiyanitsa zoyenera ndi zosayenera chifukwa choti amagwiritsa ntchito luso lawo la kuganiza.*