Machitidwe 12:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Atazindikira zimenezi, iye anapita kunyumba kwa Mariya, mayi ake a Yohane wotchedwanso Maliko.+ Kumeneko anthu ambiri anali atasonkhana nʼkumapemphera. Machitidwe 15:37 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 37 Baranaba ankafunitsitsa kuti atenge Yohane, wotchedwanso Maliko.+ Filimoni 23, 24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Epafura,+ mkaidi mnzanga mwa Khristu Yesu, akupereka moni. 24 Maliko, Arisitako,+ Dema+ ndi Luka,+ omwe ndi antchito anzanga, akuperekanso moni.
12 Atazindikira zimenezi, iye anapita kunyumba kwa Mariya, mayi ake a Yohane wotchedwanso Maliko.+ Kumeneko anthu ambiri anali atasonkhana nʼkumapemphera.
23 Epafura,+ mkaidi mnzanga mwa Khristu Yesu, akupereka moni. 24 Maliko, Arisitako,+ Dema+ ndi Luka,+ omwe ndi antchito anzanga, akuperekanso moni.