Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Machitidwe 13:4, 5
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 4 Choncho anthu amenewa, omwe anatumizidwa ndi mzimu woyera, anapita ku Selukeya ndipo kuchokera kumeneko anayenda ulendo wapamadzi kupita ku Kupuro. 5 Atafika mumzinda wa Salami anayamba kulalikira mawu a Mulungu mʼmasunagoge a Ayuda. Iwo analinso ndi Yohane yemwe ankawatumikira.*+

  • Akolose 4:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Arisitako+ mkaidi mnzanga akuti moni nonse. Komanso Maliko+ msuweni wa Baranaba, (amene ndinakulangizani kuti mumulandire+ nthawi iliyonse akadzafika kwa inu),

  • 2 Timoteyo 4:11
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 11 Luka yekha ndi amene watsala. Ubwerenso ndi Maliko chifukwa amandithandiza pa utumiki wanga.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena