Luka 1:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Inenso, popeza kuti ndafufuza zinthu zonse mosamala kwambiri kuchokera pachiyambi, ndatsimikiza kuti ndikulembereni mwatsatanetsatane, inu wolemekezeka kwambiri, a Teofilo.+ Machitidwe 1:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 1 A Teofilo, munkhani yoyamba ija, ndinalemba zinthu zonse zimene Yesu anachita ndiponso kuphunzitsa,+
3 Inenso, popeza kuti ndafufuza zinthu zonse mosamala kwambiri kuchokera pachiyambi, ndatsimikiza kuti ndikulembereni mwatsatanetsatane, inu wolemekezeka kwambiri, a Teofilo.+
1 A Teofilo, munkhani yoyamba ija, ndinalemba zinthu zonse zimene Yesu anachita ndiponso kuphunzitsa,+