Machitidwe 1:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 1 A Teofilo,+ m’nkhani yoyamba ija, ndinalemba zonse zimene Yesu anali kuchita ndi kuphunzitsa kuchokera pa chiyambi,+ Machitidwe Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 1:1 Kuchitira Umboni Mokwanira, tsa. 15 Nsanja ya Olonda,11/15/2007, tsa. 19
1 A Teofilo,+ m’nkhani yoyamba ija, ndinalemba zonse zimene Yesu anali kuchita ndi kuphunzitsa kuchokera pa chiyambi,+