Aefeso 2:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Mwamangidwa pamaziko a atumwi ndi aneneri+ ndipo Khristu Yesu ndi mwala wapakona wa mazikowo.+ Aefeso 3:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Ndikupemphanso kuti mwa chikhulupiriro chanu, mʼmitima yanu mukhale Khristu komanso chikondi.+ Muzike mizu+ ndiponso mukhale okhazikika pamaziko,+
17 Ndikupemphanso kuti mwa chikhulupiriro chanu, mʼmitima yanu mukhale Khristu komanso chikondi.+ Muzike mizu+ ndiponso mukhale okhazikika pamaziko,+