Aroma 2:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Kukhala Myuda weniweni kuli mumtima+ ndipo mdulidwe wake umakhalanso wamumtima+ wochitidwa ndi mzimu, osati ndi malamulo olembedwa.+ Munthu woteroyo amatamandidwa ndi Mulungu, osati anthu.+ Afilipi 3:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Chifukwa ife tinachita mdulidwe weniweni,+ ife amene tikuchita utumiki wopatulika motsogoleredwa ndi mzimu wa Mulungu. Timadzitamandira mwa Khristu Yesu+ ndipo sitidalira zinthu zimene anthu amaziona kuti ndi zofunika,
29 Kukhala Myuda weniweni kuli mumtima+ ndipo mdulidwe wake umakhalanso wamumtima+ wochitidwa ndi mzimu, osati ndi malamulo olembedwa.+ Munthu woteroyo amatamandidwa ndi Mulungu, osati anthu.+
3 Chifukwa ife tinachita mdulidwe weniweni,+ ife amene tikuchita utumiki wopatulika motsogoleredwa ndi mzimu wa Mulungu. Timadzitamandira mwa Khristu Yesu+ ndipo sitidalira zinthu zimene anthu amaziona kuti ndi zofunika,