1 Yohane 5:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Aliyense amene ndi mwana wa Mulungu amagonjetsa dziko.+ Ndipo chikhulupiriro chathu chatithandiza kugonjetsa dziko.+ Chivumbulutso 3:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Amene wapambana pankhondo+ ndidzamulola kuti akhale ndi ine pampando wanga wachifumu,+ ngati mmene ine ndinakhalira+ ndi Atate wanga pampando wawo wachifumu nditapambana pankhondo.
4 Aliyense amene ndi mwana wa Mulungu amagonjetsa dziko.+ Ndipo chikhulupiriro chathu chatithandiza kugonjetsa dziko.+
21 Amene wapambana pankhondo+ ndidzamulola kuti akhale ndi ine pampando wanga wachifumu,+ ngati mmene ine ndinakhalira+ ndi Atate wanga pampando wawo wachifumu nditapambana pankhondo.