1 Timoteyo 4:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Anthuwa amaletsa kukwatira,+ ndipo amalamula anthu kuti azisala zakudya+ zimene Mulungu anazilenga kuti anthu amene ali ndi chikhulupiriro+ ndiponso odziwa choonadi molondola azidya+ nʼkuyamikira Mulungu.
3 Anthuwa amaletsa kukwatira,+ ndipo amalamula anthu kuti azisala zakudya+ zimene Mulungu anazilenga kuti anthu amene ali ndi chikhulupiriro+ ndiponso odziwa choonadi molondola azidya+ nʼkuyamikira Mulungu.