1 Yohane 2:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Musamakonde dziko kapena zinthu zamʼdziko.+ Ngati wina akukonda dziko, ndiye kuti sakonda Atate.+