Yohane 11:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Atanena zimenezi, anauza ophunzira akewo kuti: “Mnzathu Lazaro ali mʼtulo,+ koma ndikupita kumeneko kukamudzutsa.” Machitidwe 7:59, 60 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 59 Pamene ankamuponya miyala, Sitefano anapempha mochonderera kuti: “Ambuye Yesu, landirani mzimu wanga.” 60 Kenako anagwada nʼkufuula ndi mawu amphamvu kuti: “Yehova,* musawaimbe mlandu wa tchimo ili.”+ Atanena zimenezi anafa.* 1 Akorinto 15:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Ndiyeno anaonekeranso kwa abale oposa 500 pa nthawi imodzi,+ ndipo ambiri a iwo tidakali nawo, koma ena anagona mu imfa.
11 Atanena zimenezi, anauza ophunzira akewo kuti: “Mnzathu Lazaro ali mʼtulo,+ koma ndikupita kumeneko kukamudzutsa.”
59 Pamene ankamuponya miyala, Sitefano anapempha mochonderera kuti: “Ambuye Yesu, landirani mzimu wanga.” 60 Kenako anagwada nʼkufuula ndi mawu amphamvu kuti: “Yehova,* musawaimbe mlandu wa tchimo ili.”+ Atanena zimenezi anafa.*
6 Ndiyeno anaonekeranso kwa abale oposa 500 pa nthawi imodzi,+ ndipo ambiri a iwo tidakali nawo, koma ena anagona mu imfa.