Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 1 Akorinto 15:22, 23
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 22 Monga zilili kuti anthu onse amafa chifukwa cha Adamu,+ anthu onse adzapatsidwanso moyo kudzera mwa Khristu.+ 23 Koma aliyense pa nthawi yoyenera: Choyamba Khristu, amene ndi chipatso choyambirira,+ kenako anthu a Khristu pa nthawi ya kukhalapo* kwake.+

  • Afilipi 3:20, 21
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 20 Koma ife ndife nzika+ zakumwamba+ ndipo tikuyembekezera mwachidwi mpulumutsi wochokera kumeneko amene ndi Ambuye Yesu Khristu.+ 21 Iye adzasintha thupi lathu lonyozekali kuti lifanane* ndi thupi lake laulemerero.+ Adzachita zimenezi pogwiritsa ntchito mphamvu zake zazikulu zimene zimamuthandiza kugonjetsa zinthu zonse kuti zikhale pansi pake.+

  • 2 Atesalonika 2:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 2 Komabe abale, pa nkhani yokhudza kukhalapo kwa Ambuye wathu Yesu Khristu+ komanso kusonkhanitsidwa kwathu kwa iye,+ tikukupemphani kuti

  • Chivumbulutso 20:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 4 Kenako ndinaona mipando yachifumu ndipo amene anakhala pamipandoyo anapatsidwa mphamvu zoweruza. Ndinaona miyoyo ya anthu amene anaphedwa chifukwa chochitira umboni za Yesu komanso chifukwa cholankhula za Mulungu. Inde, ndinaona miyoyo ya anthu amene sanalambire chilombo kapena chifaniziro chake ndipo sanalandire chizindikiro pazipumi zawo ndi padzanja lawo.+ Iwo anakhalanso ndi moyo ndipo analamulira monga mafumu limodzi ndi Khristu+ kwa zaka 1,000.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena