Yohane 17:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Ayeretseni* pogwiritsa ntchito choonadi.+ Mawu anu ndi choonadi.+ 1 Akorinto 6:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Ndipo ena a inu munali otero. Koma mwasambitsidwa kukhala oyera,+ mwapatulidwa,+ mukuonedwa ngati olungama+ mʼdzina la Ambuye wathu Yesu Khristu, komanso ndi mzimu wa Mulungu wathu. 1 Atesalonika 4:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Chifukwa Mulungu sanatiitane kuti tizichita makhalidwe odetsa, koma kuti tikhale oyera.+
11 Ndipo ena a inu munali otero. Koma mwasambitsidwa kukhala oyera,+ mwapatulidwa,+ mukuonedwa ngati olungama+ mʼdzina la Ambuye wathu Yesu Khristu, komanso ndi mzimu wa Mulungu wathu.