1 Akorinto 15:58 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 58 Choncho abale anga okondedwa, khalani olimba+ ndiponso osasunthika. Nthawi zonse muzikhala ndi zochita zambiri+ pa ntchito ya Ambuye, podziwa kuti zonse zimene mukuchita pa ntchito ya Ambuye sizidzapita pachabe.+ 1 Akorinto 16:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Khalani maso,+ khalani ndi chikhulupiriro cholimba,+ khalani olimba mtima*+ ndipo khalani amphamvu.+
58 Choncho abale anga okondedwa, khalani olimba+ ndiponso osasunthika. Nthawi zonse muzikhala ndi zochita zambiri+ pa ntchito ya Ambuye, podziwa kuti zonse zimene mukuchita pa ntchito ya Ambuye sizidzapita pachabe.+
13 Khalani maso,+ khalani ndi chikhulupiriro cholimba,+ khalani olimba mtima*+ ndipo khalani amphamvu.+