-
Agalatiya 2:7, 8Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
7 Koma ataona kuti ndapatsidwa ntchito yolalikira uthenga wabwino kwa anthu osadulidwa,+ mofanana ndi Petulo amene anapatsidwa ntchito yoti akalalikire uthenga wabwino kwa anthu odulidwa, 8 pajatu amene anapatsa Petulo mphamvu kuti akhale mtumwi kwa anthu odulidwa ndi amene anandipatsanso ine mphamvu kuti ndikhale mtumwi kwa anthu a mitundu ina.+
-