Machitidwe 22:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Koma anandiuzabe kuti, ‘Nyamuka, chifukwa ndidzakutumiza kutali kwa anthu a mitundu ina.’”+ Aroma 11:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Tsopano ndikulankhula ndi inu anthu a mitundu ina. Popeza ndine mtumwi wotumidwa kwa anthu a mitundu ina,+ ndimalemekeza utumiki wanga,+ 1 Timoteyo 2:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Chifukwa cha umboni umenewu,+ ine ndinasankhidwa kuti ndikhale mlaliki ndi mtumwi.+ Ndikunenatu zoona, sindikunama ayi. Ndinasankhidwa kuti ndiziphunzitsa anthu a mitundu ina+ za chikhulupiriro ndi choonadi.
13 Tsopano ndikulankhula ndi inu anthu a mitundu ina. Popeza ndine mtumwi wotumidwa kwa anthu a mitundu ina,+ ndimalemekeza utumiki wanga,+
7 Chifukwa cha umboni umenewu,+ ine ndinasankhidwa kuti ndikhale mlaliki ndi mtumwi.+ Ndikunenatu zoona, sindikunama ayi. Ndinasankhidwa kuti ndiziphunzitsa anthu a mitundu ina+ za chikhulupiriro ndi choonadi.