Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Machitidwe 9:15
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 15 Koma Ambuye anamuuza kuti: “Pita, chifukwa munthu ameneyu ndi chiwiya changa+ chosankhidwa chotengera dzina langa kupita nalo kwa anthu a mitundu ina+ komanso kwa mafumu+ ndi Aisiraeli.

  • Agalatiya 1:15, 16
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 15 Koma pamene Mulungu, amene anandichititsa kuti ndibadwe komanso kundiitana kudzera mu kukoma mtima kwake kwakukulu,+ anaona kuti nʼzabwino kuti 16 aulule za Mwana wake kudzera mwa ine, nʼcholinga choti ndilengeze kwa anthu a mitundu ina+ uthenga wabwino wonena za iye, sindinapite kukakambirana ndi munthu aliyense* nthawi yomweyo.

  • Aefeso 3:8
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 8 Kukoma mtima kwakukulu kumeneku kunaperekedwa kwa ine, munthu wamngʼono pondiyerekeza ndi wamngʼono kwambiri pa oyera onse.+ Ndinapatsidwa kukoma mtima kumeneku+ kuti ndilengeze kwa anthu a mitundu ina uthenga wabwino wonena za chuma chopanda polekezera cha Khristu,

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena