Machitidwe 9:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Koma Ambuye anamuuza kuti: “Pita, chifukwa munthu ameneyu ndi chiwiya changa+ chosankhidwa chotengera dzina langa kupita nalo kwa anthu a mitundu ina+ komanso kwa mafumu+ ndi Aisiraeli. Aroma 11:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Tsopano ndikulankhula ndi inu anthu a mitundu ina. Popeza ndine mtumwi wotumidwa kwa anthu a mitundu ina,+ ndimalemekeza utumiki wanga,+
15 Koma Ambuye anamuuza kuti: “Pita, chifukwa munthu ameneyu ndi chiwiya changa+ chosankhidwa chotengera dzina langa kupita nalo kwa anthu a mitundu ina+ komanso kwa mafumu+ ndi Aisiraeli.
13 Tsopano ndikulankhula ndi inu anthu a mitundu ina. Popeza ndine mtumwi wotumidwa kwa anthu a mitundu ina,+ ndimalemekeza utumiki wanga,+