Mateyu 6:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Kapolo sangatumikire ambuye awiri, chifukwa akhoza kudana ndi mmodzi nʼkukonda winayo,+ kapena angakhale wokhulupirika kwa mmodzi nʼkunyoza winayo. Simungathe kutumikira Mulungu ndi Chuma nthawi imodzi.+
24 Kapolo sangatumikire ambuye awiri, chifukwa akhoza kudana ndi mmodzi nʼkukonda winayo,+ kapena angakhale wokhulupirika kwa mmodzi nʼkunyoza winayo. Simungathe kutumikira Mulungu ndi Chuma nthawi imodzi.+