Mateyu 13:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Imene inafesedwa paminga, ndi munthu amene amamva mawu, koma nkhawa za moyo wa mʼnthawi* ino+ ndiponso chinyengo champhamvu cha chuma zimalepheretsa mawuwo kukula ndipo sabereka zipatso.+ Luka 16:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Mtumiki sangakhale kapolo wa ambuye awiri, chifukwa akhoza kudana ndi mmodzi nʼkukonda winayo, kapena angakhale wokhulupirika kwa mmodzi nʼkunyoza winayo. Simungakhale akapolo a Mulungu ndi Chuma nthawi imodzi.”+
22 Imene inafesedwa paminga, ndi munthu amene amamva mawu, koma nkhawa za moyo wa mʼnthawi* ino+ ndiponso chinyengo champhamvu cha chuma zimalepheretsa mawuwo kukula ndipo sabereka zipatso.+
13 Mtumiki sangakhale kapolo wa ambuye awiri, chifukwa akhoza kudana ndi mmodzi nʼkukonda winayo, kapena angakhale wokhulupirika kwa mmodzi nʼkunyoza winayo. Simungakhale akapolo a Mulungu ndi Chuma nthawi imodzi.”+