Machitidwe 6:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Ndiye abale, fufuzani amuna 7 pagulu lanuli a mbiri yabwino,+ amene ali ndi mzimu komanso nzeru,+ kuti ife tiwapatse udindo woyangʼanira ntchito yofunikayi.+ Tito 1:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Popeza ndi mtumiki* wa Mulungu, woyangʼanira ayenera kukhala wopanda chifukwa chomunenezera. Asakhale womva zake zokha,+ wa mtima wapachala,+ womwa mowa mwauchidakwa, wankhanza* kapena wokonda kupeza phindu mwachinyengo. 1 Petulo 5:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Wetani gulu la nkhosa za Mulungu+ zomwe zili mʼmanja mwanu. Monga oyangʼanira, muzigwira ntchito yanu, osati mokakamizika koma mofunitsitsa monga atumiki a Mulungu.+ Muziigwira ndi mtima wonse, osati chifukwa chofuna kupindulapo kenakake.+
3 Ndiye abale, fufuzani amuna 7 pagulu lanuli a mbiri yabwino,+ amene ali ndi mzimu komanso nzeru,+ kuti ife tiwapatse udindo woyangʼanira ntchito yofunikayi.+
7 Popeza ndi mtumiki* wa Mulungu, woyangʼanira ayenera kukhala wopanda chifukwa chomunenezera. Asakhale womva zake zokha,+ wa mtima wapachala,+ womwa mowa mwauchidakwa, wankhanza* kapena wokonda kupeza phindu mwachinyengo.
2 Wetani gulu la nkhosa za Mulungu+ zomwe zili mʼmanja mwanu. Monga oyangʼanira, muzigwira ntchito yanu, osati mokakamizika koma mofunitsitsa monga atumiki a Mulungu.+ Muziigwira ndi mtima wonse, osati chifukwa chofuna kupindulapo kenakake.+