Aefeso 1:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Mulungu watsegula mitima yanu nʼcholinga choti muone komanso mudziwe chiyembekezo chimene wakupatsani ndiponso zinthu zabwino kwambiri zimene walonjeza kwa oyera,+ Aheberi 10:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Ngati tikuchita machimo mwadala pambuyo podziwa choonadi molondola,+ palibenso nsembe ina imene ingaperekedwe chifukwa cha machimo athuwo.+
18 Mulungu watsegula mitima yanu nʼcholinga choti muone komanso mudziwe chiyembekezo chimene wakupatsani ndiponso zinthu zabwino kwambiri zimene walonjeza kwa oyera,+
26 Ngati tikuchita machimo mwadala pambuyo podziwa choonadi molondola,+ palibenso nsembe ina imene ingaperekedwe chifukwa cha machimo athuwo.+