Ekisodo 40:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Kenako udzabweretse Aroni ndi ana ake pafupi ndi khomo la chihema chokumanako ndipo udzawasambitse ndi madzi.+ Ekisodo 40:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Udzawadzoze ngati mmene unadzozera bambo awo+ kuti atumikire monga ansembe anga. Iwo akadzadzozedwa adzapitiriza kutumikira monga ansembe mʼmibadwo yawo yonse.”+
12 Kenako udzabweretse Aroni ndi ana ake pafupi ndi khomo la chihema chokumanako ndipo udzawasambitse ndi madzi.+
15 Udzawadzoze ngati mmene unadzozera bambo awo+ kuti atumikire monga ansembe anga. Iwo akadzadzozedwa adzapitiriza kutumikira monga ansembe mʼmibadwo yawo yonse.”+