Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Numeri 19:9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 9 Ndiyeno munthu amene si wodetsedwa awole phulusa la ngʼombeyo+ nʼkukalisiya pamalo oyera kunja kwa msasawo. Aisiraeli onse azisunga phulusalo kuti aziligwiritsa ntchito pokonza madzi oyeretsera.+ Imeneyi ndi nsembe yamachimo.

  • Numeri 19:17
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 17 Munthu wodetsedwayo amutapireko phulusa la nsembe yamachimo imene inawotchedwa ija. Phulusalo aliike mʼchiwiya nʼkuthiramo madzi akumtsinje.

  • Numeri 19:19
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 19 Munthu amene si wodetsedwa uja awaze munthu wodetsedwayo madziwo pa tsiku lachitatu komanso pa tsiku la 7.+ Ndipo pa tsiku la 7 lomwelo amuyeretse ku tchimo lake. Kenako amene akuyeretsedwayo achape zovala zake nʼkusamba ndi madzi, ndipo madzulo ake adzakhala woyera.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena